-
Malaki 1:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+
Koma inu mwanena kuti: “Mwasonyeza bwanji kuti mumatikonda?”
“Kodi Esau sanali mchimwene wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,” watero Yehova. 3 “Esau ndinadana naye.+ Mapiri ake ndinawasandutsa bwinja+ ndipo cholowa chake ndinachisandutsa malo okhala mimbulu yamʼchipululu.”+
-