Genesis 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Rabeka anali ndi mchimwene wake dzina lake Labani.+ Choncho Labani anathamanga kupita kwa munthu uja, yemwe anali kuchitsime, kunja kwa mzinda.
29 Rabeka anali ndi mchimwene wake dzina lake Labani.+ Choncho Labani anathamanga kupita kwa munthu uja, yemwe anali kuchitsime, kunja kwa mzinda.