Genesis 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Isaki anatumiza Yakobo ndipo iye ananyamuka kupita ku Padani-aramu. Anapita kwa Labani mwana wa Betuele, wa Chiaramu.+ Labaniyo anali mchimwene wake wa Rabeka+ amene anali mayi ake a Yakobo ndi Esau.
5 Choncho Isaki anatumiza Yakobo ndipo iye ananyamuka kupita ku Padani-aramu. Anapita kwa Labani mwana wa Betuele, wa Chiaramu.+ Labaniyo anali mchimwene wake wa Rabeka+ amene anali mayi ake a Yakobo ndi Esau.