Genesis 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthawi ina Isiraeli akukhala mʼdziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamngʼono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12.
22 Nthawi ina Isiraeli akukhala mʼdziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamngʼono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12.