Genesis 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, uzikhala konkuno. Ndawombeza ndipo ndapeza kuti* Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”
27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, uzikhala konkuno. Ndawombeza ndipo ndapeza kuti* Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”