Genesis 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndili ndi iwe. Ndikuyangʼanira kulikonse kumene ungapite ndipo ndidzakubwezera kudziko lino.+ Sindidzakusiya mpaka nditachita zimene ndakulonjeza.”+ Genesis 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki, inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+ Genesis 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamapeto pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ mʼdera la Kiriyati-ariba, komwe ndi ku Heburoni. Uku nʼkumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+
15 Ine ndili ndi iwe. Ndikuyangʼanira kulikonse kumene ungapite ndipo ndidzakubwezera kudziko lino.+ Sindidzakusiya mpaka nditachita zimene ndakulonjeza.”+
9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki, inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+
27 Pamapeto pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ mʼdera la Kiriyati-ariba, komwe ndi ku Heburoni. Uku nʼkumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+