Levitiko 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati mkazi akukha magazi, azikhala masiku 7 ali wodetsedwa chifukwa chakuti akusamba.+ Aliyense amene angamukhudze adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+
19 Ngati mkazi akukha magazi, azikhala masiku 7 ali wodetsedwa chifukwa chakuti akusamba.+ Aliyense amene angamukhudze adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+