1 Samueli 17:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Davide anauza Sauli kuti: “Ine mtumiki wanu ndinakhala mʼbusa wa nkhosa za bambo anga. Ndiyeno kunabwera mkango+ komanso chimbalangondo ndipo chilombo chilichonse chinagwira nkhosa.
34 Davide anauza Sauli kuti: “Ine mtumiki wanu ndinakhala mʼbusa wa nkhosa za bambo anga. Ndiyeno kunabwera mkango+ komanso chimbalangondo ndipo chilombo chilichonse chinagwira nkhosa.