Genesis 31:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndakhala mʼnyumba mwanu zaka 20. Ndakugwirirani ntchito zaka 14 kuti mundipatse ana anu aakazi awiriwa. Ndinagwiranso ntchito zaka zina 6 kuti mundipatse ziwetozi. Koma inu munkangosintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+
41 Ndakhala mʼnyumba mwanu zaka 20. Ndakugwirirani ntchito zaka 14 kuti mundipatse ana anu aakazi awiriwa. Ndinagwiranso ntchito zaka zina 6 kuti mundipatse ziwetozi. Koma inu munkangosintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+