Genesis 27:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho, Esau anayamba kudana ndi Yakobo chifukwa cha madalitso amene bambo ake anamupatsa.+ Mumtima mwake ankanena kuti: “Masiku olira maliro a bambo anga ali pafupi.+ Pambuyo pake, ndidzamupha mʼbale wanga Yakobo.”
41 Choncho, Esau anayamba kudana ndi Yakobo chifukwa cha madalitso amene bambo ake anamupatsa.+ Mumtima mwake ankanena kuti: “Masiku olira maliro a bambo anga ali pafupi.+ Pambuyo pake, ndidzamupha mʼbale wanga Yakobo.”