-
Genesis 24:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno Abulahamu anauza mtumiki wake, yemwe anali wamkulu kwambiri mʼnyumba yake komanso woyangʼanira zinthu zake zonse+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga. 3 Ndikufuna ulumbire pali Yehova, Mulungu wakumwamba ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti sutengera mwana wanga mkazi pakati pa ana aakazi a Akanani, amene ndikukhala mʼdziko lawo.+
-