5 Dzina lako silikhalanso Abulamu* koma likhala Abulahamu,* chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri. 6 Ndidzakupatsa mbadwa zambirimbiri, ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu ndi mafumu.+
13 Choncho anatenga nthambi za kanjedza nʼkutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti: “Mʼpulumutseni! Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova,*+ amene ndi Mfumu ya Isiraeli!”+