Genesis 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yakobo anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkutenga mwala umene anautsamira uja. Atatero anauimika monga mwala wachikumbutso ndipo anauthira mafuta pamwamba pake.+
18 Choncho Yakobo anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkutenga mwala umene anautsamira uja. Atatero anauimika monga mwala wachikumbutso ndipo anauthira mafuta pamwamba pake.+