Genesis 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Farao anafunsa abale ake a Yosefe aja kuti: “Kodi mumagwira ntchito yanji?” Iwo anayankha Farao kuti: “Akapolo anufe timaweta nkhosa ngati mmene ankachitira makolo athu.”+
3 Farao anafunsa abale ake a Yosefe aja kuti: “Kodi mumagwira ntchito yanji?” Iwo anayankha Farao kuti: “Akapolo anufe timaweta nkhosa ngati mmene ankachitira makolo athu.”+