Genesis 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Yuda+ anali Ere, Onani, Shela,+ Perezi+ ndi Zera.+ Koma Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+ Rute 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi,+ amene Tamara anaberekera Yuda.” 1 Mbiri 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamara,+ mpongozi wake, anamʼberekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda analipo 5. Luka 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene Yesu+ anayamba ntchito yake anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankadziwa kuti Yesu anali mwanawa Yosefe,+mwana wa Heli, Luka 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mwana wa Aminadabu,mwana wa Arini,mwana wa Hezironi,mwana wa Perezi,+mwana wa Yuda,+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
12 Ana a Yuda+ anali Ere, Onani, Shela,+ Perezi+ ndi Zera.+ Koma Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+
12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi,+ amene Tamara anaberekera Yuda.”
23 Pamene Yesu+ anayamba ntchito yake anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankadziwa kuti Yesu anali mwanawa Yosefe,+mwana wa Heli, Luka 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mwana wa Aminadabu,mwana wa Arini,mwana wa Hezironi,mwana wa Perezi,+mwana wa Yuda,+