Ekisodo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho anaika akapitawo oti aziwayangʼanira pa ntchito yawo yaukapolo kuti aziwazunza powagwiritsa ntchito mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*
11 Choncho anaika akapitawo oti aziwayangʼanira pa ntchito yawo yaukapolo kuti aziwazunza powagwiritsa ntchito mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*