13 Kumbukirani Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli atumiki anu, amene munawalumbirira powauza kuti: ‘Ndidzachulukitsa mbadwa zanu ngati nyenyezi zakumwamba+ ndipo dziko lonseli limene ndinalisankha, ndidzalipereka kwa mbadwa zanu, kuti likhale lawo mpaka kalekale.’”+