Machitidwe 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mose anabadwa pa nthawi imeneyi, ndipo Mulungu ankamuona kuti ndi wokongola. Iye analeredwa mʼnyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu.+ Aheberi 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa cha chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wooneka bwino.+ Iwo sanaope lamulo la mfumu.+
20 Mose anabadwa pa nthawi imeneyi, ndipo Mulungu ankamuona kuti ndi wokongola. Iye analeredwa mʼnyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu.+
23 Chifukwa cha chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wooneka bwino.+ Iwo sanaope lamulo la mfumu.+