Machitidwe 7:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma amene ankamenya mnzakeyo anamukankha nʼkunena kuti, ‘Ndani anakupatsa udindo woti uzitilamulira komanso kutiweruza? 28 Kodi ukufuna kundipha ngati mmene unaphera munthu wa ku Iguputo dzulo lija?’
27 Koma amene ankamenya mnzakeyo anamukankha nʼkunena kuti, ‘Ndani anakupatsa udindo woti uzitilamulira komanso kutiweruza? 28 Kodi ukufuna kundipha ngati mmene unaphera munthu wa ku Iguputo dzulo lija?’