-
Deuteronomo 16:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Musamadye nsembeyo limodzi ndi chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.+ Kwa masiku 7 muzidya mkate wopanda zofufumitsa, umene ndi mkate wamasautso, chifukwa munatuluka mofulumira mʼdziko la Iguputo.+ Muzichita zimenezi kuti muzikumbukira tsiku limene munatuluka mʼdziko la Iguputo, masiku onse a moyo wanu.+
-