Ekisodo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mkazi aliyense adzapemphe zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala kwa munthu wokhala naye pafupi ndi kwa mkazi amene akukhala mʼnyumba mwake. Zinthu zimenezi mudzaveke ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mudzatenge zinthu zambiri za Aiguputo.”+
22 Mkazi aliyense adzapemphe zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala kwa munthu wokhala naye pafupi ndi kwa mkazi amene akukhala mʼnyumba mwake. Zinthu zimenezi mudzaveke ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mudzatenge zinthu zambiri za Aiguputo.”+