Ekisodo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ndipita kuti ndikawapulumutse mʼmanja mwa Aiguputo+ ndi kuwatulutsa mʼdzikolo nʼkuwalowetsa mʼdziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+ Ekisodo 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma inu mumvere mosamala zimene ndikukulamulani lero.+ Inetu ndikuthamangitsa pamaso panu Aamori, Akanani, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
8 Choncho ndipita kuti ndikawapulumutse mʼmanja mwa Aiguputo+ ndi kuwatulutsa mʼdzikolo nʼkuwalowetsa mʼdziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
11 Koma inu mumvere mosamala zimene ndikukulamulani lero.+ Inetu ndikuthamangitsa pamaso panu Aamori, Akanani, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+