Ekisodo 12:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho muzichita chikondwerero chimenechi. Limeneli ndi lamulo kwa inu ndi kwa ana anu mpaka kalekale.+ 25 Ndipo muzidzachita mwambo umenewu+ mukadzalowa mʼdziko limene Yehova analonjeza kuti adzakupatsani.
24 Choncho muzichita chikondwerero chimenechi. Limeneli ndi lamulo kwa inu ndi kwa ana anu mpaka kalekale.+ 25 Ndipo muzidzachita mwambo umenewu+ mukadzalowa mʼdziko limene Yehova analonjeza kuti adzakupatsani.