-
Deuteronomo 7:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani+ chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse, chifukwatu mtundu wanu unali waungʼono mwa mitundu yonse.+ 8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu kuti akulanditseni mʼnyumba yaukapolo,+ mʼmanja mwa Farao* mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani, komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+
-