Numeri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza mpaka liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+ Salimo 78:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sanasunge pangano la Mulungu,+Ndipo anakana kutsatira chilamulo chake.+ Salimo 106:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mofulumira anaiwala zimene Mulungu anachita.+Sanadikire kuti Mulungu awapatse malangizo.
11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza mpaka liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+