Ekisodo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+ Numeri 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Manawo+ anali ngati mapira,*+ ndipo ankaoneka ngati utomoni woonekera mkati ngati galasi.
15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+