Genesis 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamwamba pa masitepewo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti: “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbadwa* zako.+ Genesis 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki, inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+ Mateyu 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakoboʼ?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+ Machitidwe 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ine ndine Mulungu wa makolo ako, Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo.’+ Mose anayamba kunjenjemera ndipo sanafunenso kupita pafupi ndi chitsambacho kuti akaonetsetse.
13 Pamwamba pa masitepewo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti: “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbadwa* zako.+
9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki, inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+
32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakoboʼ?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+
32 ‘Ine ndine Mulungu wa makolo ako, Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo.’+ Mose anayamba kunjenjemera ndipo sanafunenso kupita pafupi ndi chitsambacho kuti akaonetsetse.