Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+ Salimo 95:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa Yehova ndi Mulungu wamkulu,Iye ndi Mfumu yaikulu kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 97:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa inu Yehova, ndinu Wamʼmwambamwamba woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.Ndinu wokwezeka kwambiri kuposa milungu ina yonse.+
11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+
9 Chifukwa inu Yehova, ndinu Wamʼmwambamwamba woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.Ndinu wokwezeka kwambiri kuposa milungu ina yonse.+