Ekisodo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mose anakhala mʼbusa wa ziweto za Yetero*+ apongozi ake, wansembe wa ku Midiyani. Pamene ankaweta ziwetozo chakumadzulo kwa chipululu, anafika kuphiri la Mulungu woona, ku Horebe.+ Ekisodo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Mulungu anati: “Ndidzakhala nawe,+ ndipo chizindikiro chosonyeza kuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi: Pambuyo potulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira* Mulungu woona paphiri lino.”+
3 Mose anakhala mʼbusa wa ziweto za Yetero*+ apongozi ake, wansembe wa ku Midiyani. Pamene ankaweta ziwetozo chakumadzulo kwa chipululu, anafika kuphiri la Mulungu woona, ku Horebe.+
12 Pamenepo Mulungu anati: “Ndidzakhala nawe,+ ndipo chizindikiro chosonyeza kuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi: Pambuyo potulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira* Mulungu woona paphiri lino.”+