Deuteronomo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu, ngakhale kumwamba kwa kumwambako* komanso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zonsezo ndi zake.+
14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu, ngakhale kumwamba kwa kumwambako* komanso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zonsezo ndi zake.+