Deuteronomo 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati mʼbale wanu anagulitsidwa kwa inu, kaya ndi mwamuna kapena mkazi wa Chiheberi, ndipo wakutumikirani zaka 6, mʼchaka cha 7 muzimumasula nʼkumulola kuti achoke.+
12 Ngati mʼbale wanu anagulitsidwa kwa inu, kaya ndi mwamuna kapena mkazi wa Chiheberi, ndipo wakutumikirani zaka 6, mʼchaka cha 7 muzimumasula nʼkumulola kuti achoke.+