-
Genesis 9:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kuwonjezera pamenepo, aliyense amene adzakupheni* ndidzamupatsa chilango. Ngati chamoyo chilichonse chapha munthu, chamoyocho chidzaphedwanso. Ndipo munthu aliyense wochotsa moyo wa mʼbale wake, ndidzamupatsa chilango.+ 6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+
-