Genesis 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwonjezera pamenepo, aliyense amene adzakupheni* ndidzamupatsa chilango. Ngati chamoyo chilichonse chapha munthu, chamoyocho chidzaphedwanso. Ndipo munthu aliyense wochotsa moyo wa mʼbale wake, ndidzamupatsa chilango.+ Numeri 35:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndi amene amadetsa dziko.+ Ndipo dziko limene ladetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe ndi china chilichonse, kupatulapo magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+
5 Kuwonjezera pamenepo, aliyense amene adzakupheni* ndidzamupatsa chilango. Ngati chamoyo chilichonse chapha munthu, chamoyocho chidzaphedwanso. Ndipo munthu aliyense wochotsa moyo wa mʼbale wake, ndidzamupatsa chilango.+
33 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndi amene amadetsa dziko.+ Ndipo dziko limene ladetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe ndi china chilichonse, kupatulapo magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+