-
Deuteronomo 22:28, 29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ngati mwamuna wakumana ndi namwali amene sanalonjezedwe ndi mwamuna kuti adzamukwatira ndipo wamugwira nʼkugona naye, ndiyeno agwidwa,+ 29 mwamunayo azipereka masekeli 50 asiliva kwa bambo a mtsikanayo, ndipo azikhala mkazi wake.+ Chifukwa chakuti wamuchititsa manyazi, sadzaloledwa kumusiya masiku onse a moyo wake.
-