Salimo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mudzaweruza mwachilungamo mwana wamasiye komanso anthu oponderezedwa,+Kuti munthu wamba wochokera kufumbi asadzawachititsenso mantha.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+
18 Mudzaweruza mwachilungamo mwana wamasiye komanso anthu oponderezedwa,+Kuti munthu wamba wochokera kufumbi asadzawachititsenso mantha.+
4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+