Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukathamangitse anthu onse amene akukhala mʼdzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala+ ndi mafano awo onse achitsulo*+ komanso mukagwetse malo awo onse opatulika.+
52 Mukathamangitse anthu onse amene akukhala mʼdzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala+ ndi mafano awo onse achitsulo*+ komanso mukagwetse malo awo onse opatulika.+