Ekisodo 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Mose anakhalabe mʼphirimo ndi Yehova masiku 40, masana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Malamulo Khumi,* pamiyala yosemayo.+ Deuteronomo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditakwera mʼphiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita ndi inu,+ ndinakhala mʼphirimo masiku 40, masana ndi usiku,+ ndipo sindinadye chakudya kapena kumwa madzi.
28 Choncho Mose anakhalabe mʼphirimo ndi Yehova masiku 40, masana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Malamulo Khumi,* pamiyala yosemayo.+
9 Nditakwera mʼphiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita ndi inu,+ ndinakhala mʼphirimo masiku 40, masana ndi usiku,+ ndipo sindinadye chakudya kapena kumwa madzi.