Numeri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu nʼkuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira+ zake zozimitsira nyale, zoikamo phulusa la zingwe za nyale ndi ziwiya zake zonse zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse.
9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu nʼkuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira+ zake zozimitsira nyale, zoikamo phulusa la zingwe za nyale ndi ziwiya zake zonse zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse.