Ekisodo 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako utenge zovala+ zija nʼkuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi. Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa komanso umumange lamba* woluka wa efodi mʼchiuno mwake.+ Levitiko 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero anaveka Aroni mkanjo+ nʼkumumanga lamba wapamimba.*+ Anamuvekanso malaya odula manja+ komanso efodi+ ndipo anamanga lamba woluka+ wa efodiyo.
5 Kenako utenge zovala+ zija nʼkuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi. Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa komanso umumange lamba* woluka wa efodi mʼchiuno mwake.+
7 Atatero anaveka Aroni mkanjo+ nʼkumumanga lamba wapamimba.*+ Anamuvekanso malaya odula manja+ komanso efodi+ ndipo anamanga lamba woluka+ wa efodiyo.