16 Ndiye pita ukasonkhanitse akulu a Isiraeli nʼkuwauza kuti, ‘Yehova Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, anaonekera kwa ine nʼkundiuza kuti: “Ndithu, ndaona zimene zikukuchitikirani+ komanso ndaona zimene akukuchitirani ku Iguputo.