Mateyu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya mzimu wa Mulungu, ndiye kuti Ufumu wa Mulungu wakufikirani modzidzimutsa.+ Luka 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi chala cha Mulungu,+ ndiye kuti Ufumu wa Mulungu wakufikirani modzidzimutsa.+ 2 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo atumiki a Mulungu.+ Kalatayo si yolembedwa ndi inki koma ndi mzimu wa Mulungu wamoyo. Si yolembedwa pazolembapo zamiyala+ koma mʼmitima.*+
28 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya mzimu wa Mulungu, ndiye kuti Ufumu wa Mulungu wakufikirani modzidzimutsa.+
20 Koma ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi chala cha Mulungu,+ ndiye kuti Ufumu wa Mulungu wakufikirani modzidzimutsa.+
3 Chifukwa zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo atumiki a Mulungu.+ Kalatayo si yolembedwa ndi inki koma ndi mzimu wa Mulungu wamoyo. Si yolembedwa pazolembapo zamiyala+ koma mʼmitima.*+