Numeri 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiwagwetsera mliri ndi kuwawononga, ndipo iwe ndidzakusandutsa mtundu waukulu ndi wamphamvu kuposa iwowa.”+ Deuteronomo 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndisiye kuti ndiwawononge nʼkufafaniza dzina lawo pansi pa thambo, ndipo ndikupange iweyo kukhala mtundu wamphamvu komanso waukulu kwambiri kuposa iwowo.’+
12 Ndiwagwetsera mliri ndi kuwawononga, ndipo iwe ndidzakusandutsa mtundu waukulu ndi wamphamvu kuposa iwowa.”+
14 Ndisiye kuti ndiwawononge nʼkufafaniza dzina lawo pansi pa thambo, ndipo ndikupange iweyo kukhala mtundu wamphamvu komanso waukulu kwambiri kuposa iwowo.’+