Deuteronomo 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno ndinatenga mwana wa ngʼombeyo, amene munachimwa chifukwa chomupanga,+ ndipo ndinamuwotcha pamoto. Kenako ndinamuphwanya, nʼkumupera mpaka kukhala wosalala ngati fumbi, ndipo ndinawaza fumbilo mumtsinje umene unkachokera mʼphirimo.+
21 Ndiyeno ndinatenga mwana wa ngʼombeyo, amene munachimwa chifukwa chomupanga,+ ndipo ndinamuwotcha pamoto. Kenako ndinamuphwanya, nʼkumupera mpaka kukhala wosalala ngati fumbi, ndipo ndinawaza fumbilo mumtsinje umene unkachokera mʼphirimo.+