-
Numeri 11:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Yehova anayankha Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 pakati pa akulu a Isiraeli, amene umawaona* kuti ndi akulu komanso oyangʼanira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi ndi iwe. 17 Ine ndibwera kumeneko+ kudzalankhula nawe+ ndipo ndidzatenga gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe nʼkuuika pa anthuwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyangʼanira anthuwo, kuti usausenze wekha.+
-