Numeri 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chonde, khululukani zolakwa za anthuwa mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika chomwe ndi chachikulu, ngati mmene mwakhala mukuwakhululukira kuchokera ku Iguputo mpaka pano.”+
19 Chonde, khululukani zolakwa za anthuwa mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika chomwe ndi chachikulu, ngati mmene mwakhala mukuwakhululukira kuchokera ku Iguputo mpaka pano.”+