34 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Utenge muyezo wofanana wa zinthu zonunkhira izi:+ madontho a sitakate, onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani weniweni. 35 Zinthu zimenezi upangire zofukiza.+ Usakanize zonunkhiritsa zimenezi mwaluso, uthire mchere,+ zikhale zoyera ndi zopatulika.