Genesis 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Abele anabweretsa ana oyamba a ziweto zake+ nʼkuwapereka nsembe, ndipo anaperekanso nsembe mafuta a ziwetozo. Yehova anasangalala ndi Abele komanso nsembe yake.+
4 Koma Abele anabweretsa ana oyamba a ziweto zake+ nʼkuwapereka nsembe, ndipo anaperekanso nsembe mafuta a ziwetozo. Yehova anasangalala ndi Abele komanso nsembe yake.+