-
Ekisodo 22:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ngati munthu wapatsa mnzake bulu, ngʼombe, nkhosa kapena chiweto chilichonse kuti amusungire, ndipo chafa kapena chavulala kwambiri kapenanso chagwidwa popanda munthu kuona zimene zachitika, 11 amene anasunga zinthuzo azilumbira kwa mnzake pamaso pa Yehova kuti sanachite zimenezo pa katundu wa mnzake. Mwiniwake wa katunduyo azivomereza lumbirolo ndipo mnzakeyo asamalipire.+
-