Numeri 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uzilidyera mʼmalo oyera koposa,+ ndipo mwamuna aliyense wa fuko lanu angathe kudya nawo. Gawo limenelo lizikhala chinthu chopatulika kwa iwe.+
10 Uzilidyera mʼmalo oyera koposa,+ ndipo mwamuna aliyense wa fuko lanu angathe kudya nawo. Gawo limenelo lizikhala chinthu chopatulika kwa iwe.+