-
2 Mbiri 29:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Kenako Hezekiya anati: “Tsopano popeza mwapatulidwa kuti muzitumikira Yehova, bweretsani nsembe zoyamikira ndi nsembe zina kunyumba ya Yehova.” Ndiyeno gulu la anthuwo linayamba kubweretsa nsembe zoyamikira ndi nsembe zina, ndipo aliyense amene anali ndi mtima wofunitsitsa anabweretsa nsembe zopsereza.+
-